Ophunzira pa UNIMA akhazikitsa kampani ya luso lamakono
Ophunzira pa sukulu yaukachenjede ya University of Malawi(Unima) ku Zomba akhazikitsa chipangizo chothandiza anthu omwe ali ndi ulumali wosaona. Mmodzi mwa ophunzirawo, Hudson Mwangalika, wati

