Category : Local
Kambwiri ayikidwa mmanda mawa
Thupi la amene anali mkhalakale pa nkhani zoulutsa mawu, Joshua Kambwiri, alitengera ku mudzi kwawo ku Domasi m’boma la Zomba, kumene akaliyike m’manda mawa Lolemba....
Voting commences in the UTM elective convention
Voting has started in the UTM elective convention underway in Mzuzu. The four presidential candidates Dalitso Kabambe, Mathews Mtumbuka, Patricia Kaliati and Newton Kambala have...
Osakhala, kuchita malonda pafupi ndi njanji — Boma
Boma lati anthu okhala komanso ochita malonda kufupi ndi njanji ali ndi udindo oteteza zipangizo za njanji kuti ntchito za sitima zipite patsogolo m’dziko muno....
Oimba aphunzire kugwira ntchito ndi aluso ena — Billy Kaunda
Billy Kaunda walangiza oimba kuti aphunzire kugwira ntchito ndi aluso ena monga alakatuli. Kaunda wayankhula izi pomwe wati akubwera ndi chimbale chatsopano posachedwapa momwe Okoma...
Boma likuyika maziko a chitukuko — Dr Chakwera
Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera wati boma likuyika maziko okhazikika oti apindulire dziko lino kuyambira panopa mpakana mibadwo yamtsogolo. Dr Chakwera amayankhula izi...
4 years in prison for theft of cattle
Chikwawa First Grade Magistrate’s court has convicted and sentenced John Justin to 4 years in prison for stealing cattle worth over K1 million from a...

