Anthu amunzinda wa Blantyre anali okondwa kwambiri ataonelera maimbidwe ochititsa chidwi kuchoka kwa oimba wa chamba cha amapiano, Young Stunna, wochokera m’dziko la South Africa....
Oyimba nyimbo za uzimu ati ndi okondwa ndi momwe nzika za mu nzinda wa Lilongwe zinabwelera pa phwando la maimbidwe limene linachitikira ku Sheaffer lolemba...
Katswiri oyimba amene amachokera m’boma la Phalombe, Giboh Pearson, wapulumuka pa ngozi ya galimoto yomwe wachita pomwe amapita ku phwando la msangulutso ku Bangwe mu...
Charles Sinetre ndimmodzi wa akatswiri amene adayimba limodzi ndi malemu Lucius Banda. Kodi adzamukumbukira motani? Olembankhani wathu Simeon Boyce anacheza ndi Sinetre motere: Q-Kodi ndi...
Yemwe amakhala pafupi ndi nyumba ya malemu “soldier” Lucius Banda m’boma la Balaka, Ras Jonah, yemwe dzina lake lenileni ndi Ronald Chigwale, wati mu nyimbo...
President Dr Lazarus Chakwera has paid tribute to legendary artist ‘soldier’ Lucius Banda, who before his demise on Sunday served as the Presidential Advisor on...
M’modzi mwa akatswiri oyimba nyimbo za Hip-hop komanso katakwe paza Graphic Designing, Kennedy Mwenya, yemwe amatchuka kuti Spiral, wamwalira pangozi ya galimoto ku Mzuzu. Malipoti...
Woimba wachichepere Sife Mw, yemwe dzina lake lenileni ndi Silvia Sifenjanie Sande ndipo ali ndi zaka 21, wati nyimbo yake yatsopano ndi bvumbulutso loti litonthoze...
Oyimba nyimbo za chamba cha Amapiano, Christopher ‘Avokado’ Malera wayamika Mulungu pomupulumutsa pa ngozi ya galimoto yomwe idachitika Lachiwiri m’mawa ku Mvera m’boma la Dowa....
South African singer, Young Stunna, will jet in the country on Saturday, 25 May 2024, to perform at Beerland Festival music concert, which will take...