President Chakwera apitiliza ulendo m’chigawi cha ku m’mawa
Popitiriza ndi ulendo wake m’chigawo chakummawa kwa dziko lino, Prezidenti Dr Lazarus Chakwera lero ayendera chitukuko chosiyanasiyana m’boma la Balaka. Mtsogoleri wadziko linoyu ayendera Demeter...

