The number of Social Cash Transfer Programme beneficiaries in Mzimba District is set to rise from the current 13,800 to 21000. Deputy Director Responsible for...
Thupi la wachiwiri kwa mtsogoleri wadziko lino, malemu Dr Saulos Chilima, aliyika m’manda pamudzi wa Mbirimtengelenji pa Nsipe m’dera la Senior Chief Inkosi Champiti m’boma...
Oyimira akubanja kwa mayi Mary Chilima, bambo Ziliro Chiwambo, anati akuyamika mtsogoleri wa dziko lino komanso aMalawi chifukwa cha chikondi chomwe aonetsa pa zovutazi. Iwo...
Nduna yazofalitsa nkhani yalengeza kusintha kwina kwa ndondomeko ya momwe mwambo wa maliro a Dr Saulos Chilima uyendere. Mwa zina, a Kunkuyu ati mtsogoleri wa...
Mtsogoleri wa dziko lino, Dr.Lazrus Chakwera, akhala nawo pamwambo wa nsembe ya Misa ya mayi Shanil Dzimbiri kunyumba ya chisoni ya Sunrise ku Kanengo munzinda...
President Dr Lazarus Chakwera has urged the international community to assist in investigating the plane crash that claimed the lives of Vice President Dr Saulos...
Anthu ochuluka asonkhana ku nyumba ya chisoni ya Sunset Funeral Services ku Kanengo munzinda wa Lilongwe komwe pali chikonzero chonyamula ena mwa matupi a anthu...
FIFA President Gianni Infantino has offered his condolences to madam Mary Chilima, wife to the Vice President, late Dr Saulos Chilima, at their Area 12...