‘Tikusowekera chakudya, zipangizo zophunzitsira ntchito za manja’
M’busa Thomson John Chipeta, yemwe anakhazikitsa Home of Hope Orphanage, m’boma la Mchinji wati mabvuto akulu omwe akukumananawo ndi kuchepa kwa chakudya komanso zipangizo zophunzitsira

