Tsimikizirani anthu kuti maziko onse achitukuko apindulira aliyense- Dr. Chakwera
Mtsogoleri wadziko lino, Dr. Lazarus Chakwera, walonjeza kuti boma lake lionetsetsa kuti maziko onse achitukuko, amene akuchitika pakadali pano, apindulire aliyense. Dr. Chakwera walankhula izi

