People from the area of Traditional Authority Nkaya in Balaka have applauded Balaka District Council for the construction of a K93 million health post, which...
Apolisi m’chigawo chakummwera amanga Richard Herema wazaka 42, yemwe kwawo ndi ku Mozambique, pomuganizira kuti iyeyo pamodzi ndi amzake,l anathyola nyumba ziwiri ndikuba ndalama zoposa...
Apolisi mu mzinda wa Zomba amanga a Andrew Banda a zaka 25 zakubadwa powaganizira kuti anagwirira mwana wazaka 12. Ofalitsankhani wa Polisi ya Zomba, a...
Malawi Broadcasting Corporation (MBC) and the Media Institute of Southern Africa (MISA) Malawi Chapter have extended their condolences to the family of the late Geoffrey...
Khothi la Magistrate mu mzinda wa Blantyre la lamula kuti abambo atatu akagwire ukayidi kwa zaka ziwiri komanso chaka ndi theka kaamba kopezeka olakwa pochita...
Bwalo la Milandu la High Court mumzinda wa Lilongwe lathetseratu mlandu wa pakati pa ochita malonda a ku Nsungwi, Area 25 ndi m’mwenye Akbar Salahudding...
Nduna yoona za madzi komanso ukhondo, mayi Abida Mia, pamodzi ndi anthu ena ambiri, asonkhana ku Machinjiri Area 3 mu mzinda wa Blantyre kumene akukhuza...
Mawanja oposa makumi awiri ku Choma mu mzinda wa Mzuzu ati ali ndi chiyembekezo kuti ulimi wa nkhuku omwe bungwe la SOS lawathandiza uli ndikuthekera...
Anthu ochita malonda ochokela ku Nsungwi ku Area 25 mu mzinda wa Lilongwe asonkhana panja pa bwalo la High Court kumene akuyembekezera kuti amve chigamulo...