Ana aphunzitsidwe njira zodzitetezera ku nkhanza zogwiliridwa
Ena mwa akatswiri oona zamalingaliro m’dziko muno ati pakufunika maphunziro ozindikiritsa ana osaposera zaka 13 momwe angadzitetezere kum’chitidwe wankhanza zogonana poyang’anira kukula kwa m’chitidwewu m’dziko...

