Malawi Broadcasting Corporation
Entertainment Entertainment Local Local News

Tipereke mpata kwa ena opata mphoto – Mandota

Katswiri ochita zisudzo, Jamil Chikakuda, yemwe amadziwika bwino ndi dzina loti Che Mandota, wati sakufuna kutenga nawonso gawo mu mphotho zosiyanasiyana zimene aluso amapatsidwa m’dziko muno pa chaka kaamba kaluso lawo.

Che Mandota wati akufuna kupereka mpata kwa aluso ena kaamba kakuti iye anatenga mphoto zonse zimene waluso angakhumbire kutenga m’dziko muno.

Kulengezaku kwadza patangopita masiku owerengeka Zeze Kingston nayenso atalengeza ganizo ngati lomweli.

 

Related posts

CYCLONE SCARS A MOTIVE FOR REFORESTATION – OLD MUTUAL

Rabson Kondowe

Mayi akagwira ukayidi kwa zaka ziwiri atavulaza mamuna wake

Romeo Umali

Land dispute case adjourned to September

MBC Online
error: All Content is protected. Copyright © 2022. Malawi Broadcasting Corporation. All Right Reserved.