Malawi Broadcasting Corporation
Local News Nkhani

Anamalira akhamukira ku CI

Mwambo wa mapemphero otsanzikana ndi katswiri pa zamalamulo Ralph Kasambara wayamba ku CI mu mzinda wa Blantyre.

Akuluakulu osiyanasiyana kuphatikizapo a boma, a zipani za ndale komanso mipingo, ali nawo pa mwambowu.

Thupi la a Kasambara ayenda nalo pa ndege kupita ku NkhataBay masana ano ukangotha mwambowu.

 

Related posts

PPPC concludes Investor Conference

Rabson Kondowe

Six political parties adopt code of conduct

Rabson Kondowe

Mafumu apempha boma, mabungwe athandize Zoe Foundation

Alinafe Mlamba
error: All Content is protected. Copyright © 2022. Malawi Broadcasting Corporation. All Right Reserved.