Mfumu yaikulu Mkukula yayamika boma kaamba ka chitukuko cha madzi ammipopi
Mfumu yaikulu Mkukula ya m’boma la Dowa yayamika boma chifukwa chowapatsa anthu akwa Mkukula chitukuko cha madzi a m’mipopi. Mfumuyi yati m’mbuyomu anthu mderali amavutikira...

