Aliyense apindula ndi ntchito zachitukuko cha boma- Chimwendo Banda
Nduna ya maboma ang’ono, Richard Chimwendo Banda, yati boma lipitiriza kuonetsetsa kuti miyoyo ya anthu ammadera akumidzi ikusintha kudzera mu ntchito zachitukuko. Ndunayi yanena izi...

