Achinyamata adziwe kufunika kolembetsa mkaundula wa voti – Mumba
				Mmodzi mwa anthu odziwika bwino pandale, a Vitumbiko Mumba, wati nthawi yakwana yoti achinyamata azindikire kufunika kolembetsa mkaundula wavoti ndikutenga nawo gawo pankhani zandale m’dziko			
			
			
		
