GEFT ichepetsa mavuto obwera ndi kusintha kwa nyengo — Boma, UNDP
Boma, molumikizana ndi bungwe la UNDP, lakhazikitsa ntchito ya gawo lachiwiri komanso lachitatu ya Green Economic Transformation Facility (GETF). Ntchitoyi ikupereka danga kwa anthu komanso...