Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, Dr Michael Usi, afika ku ofesi ya Bwanamkubwa wa boma la Thyolo pa ulendo wawo oyendera ntchito za boma mwadzidzidzi.
Iwo afika nthawi itangokwana kota pasiti seveni (7:15) m’mawa uno.
Pakadali pano, DC wa boma la Thyolo, a Hudson Kuphanga, akufotokozera a Usi ntchito zomwe zikugwiridwa m’bomalo.