Dziko la Malawi latsegula ofesi ya ukazembe m’dziko la Israel kaamba kofuna kuti dziko lino lipindule ndi ntchito za ulimi ndi mtengatenga, mwa zina. A...
President Dr Lazarus Chakwera has expressed gratitude and extended best wishes to artists across the country as they commemorate World Art Day. In a special...
President Dr Lazarus Chakwera will undertake several activities in Kasungu tomorrow, Monday. He will inaugurate the Tobacco Commission House in Senior Chief Kaomba’s area and...
Bungwe la asilamu la Muslim Association of Malawi (MAM) lati mwezi otsiriza kusala kudya wa Ramadan sunaoneke, choncho iwo ati Eid idzakhalapo lachinayi. Mneneri wa...
Chinthuzi: tsamba la Mtukula Pakhomo Anthu okhala mu mzinda wa Blantyre, amene boma linawayika pa mndandanda wa mtukula pakhomo wammizinda, lero alandira ndalama zawo zokwana...
Chiwerengero cha anthu omwe amwalira atamwa mowa odziwika kuti ‘ambuye tengeni’ kwa Manase ku Blantyre tsopano chafika pa asanu ndi atatu 8. Apolisi atsimikiza kuti...
Mkulu wa zaumoyo ku Blantyre, Dr Gift Kawalazira, ati anthu enanso awiri amwalira, kufikitsa chiwerengero cha anthu omwe afa atamwa mowa umene ukudziwika ndi dzina...
Jonathan Phillipo, mneneri wa Polisi ku Chileka Apolisi ku Chileka amanga bambo McLean Luka a zaka 24 omwe athandiza kuchiritsa okha mkazi wawo yemwe anali...
Phungu wadera la Blantyre City East, a John Bande, wapempha mafumu kuti akhale patsogolo poteteza zipangizo ndi katundu wa boma pomwe akulimbikitsa ntchito zachitukuko. A...