Category : Local
VP to attend Human Resource Society of Malawi AGM
Vice President Dr Michael Usi is scheduled to preside over the official opening of the 2024 Human Resource Society of Malawi Annual General Conference in...
Actallliance launches El Niño Response in Lower Shire
A consortium of Christian development organizations, Actalliance, has initiated a six-month disaster response programme in Chikwawa and Nsanje. The project aims to provide cash transfers...
Chakwera to preside over Mzuzu University’s 26th Congregation
President Dr Lazarus Chakwera, who also serves as the Chancellor of Mzuzu University, will preside over the First Session of the 26th Congregation at the...
Ndilimbikitsa ntchito zachitukuko — Mwase
Khansala wapampando watsopano m’dera la Mwasa ku Mangochi, a Stewart Mwase, alonjeza kuti alimbikitsa ntchito zachitukuko zomwe anaziyamba kale pa nthawi yomwe asanasankhidwe pa udindowu....
Kamtukule alowa chipani cha MCP
Nduna ya zokopa alendo a Vera Kamtukule omwe anali achipani cha UTM alowa chipani cha Malawi Congress. Powalandira mchipanichi Mlembi Wamkulu mchipani cha MCP a...
Tsogolo la mlandu wa a Mbedza lioneka masana ano
Masana ano bwalo la Magistrate mnzinda wa Lilongwe likuyembezeka kupereka chigamulo pa pempho labelo lomwe oyimira a Chiyanjano Mbedza anapereka sabata yatha. A Mbedza anawamanga...
MCP yayamikira anthu aku Mangochi powakhulupilira
Wapampando wa chipani cha Malawi Congress (MCP) m’chigawo chapakati a Zebron Chilondola ayamikira anthu a m’boma la Mangochi kaamba kowonetsa chikhulupiliro mu chipanichi. A Chilondola...
Mfumu Mponela yakhutira ndi chitukuko cha msewu wa M1
Mfumu yaikulu Mponela yayamika mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera kaamba ka ntchito yokonzanso msewu wa M1 omwe udaonongeka kwambiri. Inkosi Mponela yanena zimenezi...
Alimi ku Mtengowanthenga ayamikira boma pa mitengo ya fodya
Khwimbi la anthu lasonkhana pa Mtengowanthenga m’boma la Dowa, pamene akudikila mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera, kuti awalankhule pamene iye akudutsa pa ulendo...

