Category : Local
ActionAid hands 12 motorcycles to health project partners
ActionAid Malawi has donated 12 motorcycles worth K156 million to CRECCOM, the Catholic Health Commission (CHC), and the Malawi Network of People Living with HIV/AIDS...
Mwambo wa Sand Music siukhalapo chaka chino
Mwambo wa Sand Music Festival wa chaka chino siukhalapo chifukwa cha imfa ya ‘Soldier’ Lucius Banda, amene anali mkulu wa kampani imene imakonza mwambowu ya...
Anthu aku Mangochi akondwa ndi kusindikiza zitupa zoyendera
Anthu ambiri m’boma la Mangochi ndi maboma ena a m’chigawo cha kumvuma akondwera ndi kuyambanso kwa ntchito yopanga zitupa zoyendera zomwe ikuchita nthambi ya Immigration...
Learner mentors making a difference in Mchinji Schools
Young girls from Mchinji District have urged the youth to stay in school and pursue their dreams. The girls, who are acting as mentors, have...
Men advised to refrain from shunning NICE meetings in Likoma
District Programmes Officer (DPO) for National Initiative for Civic Education (NICE) for Likoma District, Blessings Mahata, has advised men to refrain from shunning NICE meetings...
Bungwe la FAO lithandiza dziko la Malawi
Bungwe loona zachakudya padziko lonse la FAO lati lipitiriza kugwila ntchito ndi dziko la Malawi powonetsetsa kuti boma likwaniritse masomphenya ake owonetsetsa kuti anthu ali...
MEC yalengeza zotsatira za chisankho cha komiti yayikulu ya DPP
Bungwe loyendetsa zisankho m’dziko muno la Malawi Electoral Commission (MEC) yalengeza zotsatira za chisankho cha komiti yaikulu ya chipani cha Democratic Progressive. A Joseph Mwanamvekha...
Bungwe la MEC layamba kuonkhetsera zotsatira za chisankho kumsonkhano waukulu wachipani cha DPP
Akuluakulu a bungwe loona zachisankho mdziko muno la Malawi Electoral Commission (MEC) ayamba ntchito yoonkhetsera ma voti omwe nthumwi ku msonkhano waukulu wachipani cha DPP...
UTM yalimbikitsa achinyamata
Chipani cha UTM chalimbikitsa achinyamata kuti alembetse mu kaundula wa unzika kuti adzakhale ndi mwai oponya nawo voti pachisankho chachikulu chomwe chichitike mdziko muno chaka...

