‘World Bank ili ndi chikhulupiliro mu utsogoleri ku Malawi’
Mmodzi wa ounikira nkhani za utsogoleri wabwino, Undule Mwakasungula, wayamikira mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera, pobweretsa chikhulupiliro mwa a World Bank pamene yapereka

