Atsogoleri a zipembedzo alimbikitsa umodzi pa chikumbutso
Atsogoleri azipembedzo zosiyanasiyana alimbikitsa umodzi pakati pa aMalawi, pomwe patha chaka chimodzi dziko lino litakumana ndi namondwe wa Freddy. Ena mwa alalikiwa ndi Phophet Shepherd

