Anthu aku Ntcheu ayamika boma chifukwa cha ngongole ya K2.1 billion kwa alimi
Senior Chief Mpando yakwa Kambilonjo ku Ntcheu, yayamika boma chifukwa chopereka ngongole yokwana K2.1 billion kwa anthu m’bomali kudzera ku NEEF. Pomulandira President Chakwera, Senior...

