Malawi Broadcasting Corporation
Uncategorized

Mwezi sunaoneke, tchuthi lachinayi —MAM

Bungwe la asilamu la Muslim Association of Malawi (MAM) lati mwezi otsiriza kusala kudya wa Ramadan sunaoneke, choncho iwo ati Eid idzakhalapo lachinayi.

Mneneri wa bungweli, Sheikh Dinala Chabulika, auza MBC kuti zateremu ndiye kuti asilamu atsiriza kusala kudya mawa lachitatu ndipo tchuthi cha Eid chidzachitika lachinayi likudzali.

Related posts

CHAKWERA HIRES NEW CABINET

McDonald Chiwayula

Zomba Council throws LAPA Party

Alinafe Mlamba

Nkhotakota to host 2024 Lake of Stars

Alinafe Mlamba
error: All Content is protected. Copyright © 2022. Malawi Broadcasting Corporation. All Right Reserved.