Malawi Beach Soccer Association has urged national beach soccer players to take advantage of the beach league, which starts next week, to improve their performance...
Bungwe la Action Aid lati likambirana ndi boma kuti lithandize sukulu ya pulayimale ya John C. Thomas kumene kabweredwe ka ophunzira kasintha kutsatira kuthetsa kuphika...
Wachiwiri watsopano kwa mtsogoleri wa dziko lino, Dr Michael Usi, wati adzipereka kwathunthu kuthandiza Prezidenti Dr Lazarus Chakwera potukula dziko lino komanso kukweza aMalawi. Iwo...
Anthu ena alipanja pa nyumba ya malamulo pomwe ayika kanema pofuna kupereka mwayi kwa anthuwo oonelera mwambo wolumbilitsa Dr Michael Bizwick Usi kukhala wachiwiri kwa...
Guinea-Bissau President Umaro Sissoco Embalo has left the country through Kamuzu International Airport. While in the country, President Embaló offered his condolences to President Dr...
Premier Bet, through its Premier Projects initiative, has installed new plastic flooring at the Blantyre Youth Centre netball court and handed it over to the...
Mtsogoleri wa dziko la Guinea-Bissau a Umaro Sissoco Embalo afika m’dziko lino mawa Lachisanu kudzapepesa imfa ya amene wachiwiri kwa m’tsogoleri wa dziko lino Dr...
President Dr Lazarus Chakwera has appointed Dr Michael Bizwick Usi as the country’s Vice President with immediate effect. In a statement from the Secretary to...
President of Guinea-Bissau Sissoco Embalo will visit Malawi tomorrow Friday, 21st June 2024 A statement released by the Office of the Secretary for Foreign Affairs...