Malawi Broadcasting Corporation
Nkhani

WAIPHULA!

Mnyamata wa zaka 20  wa ku Lilongwe, wapeza mphoto ya ndalama zokwana K174.2 million  atasewera masewero oulutsa ndege ndi BetPawa.

Akuluakulu a kampaniyi atsimikiza izi ku Blantyre komwe mwambo olengeza za mnyamatayu unachitika.

Mu mbiri ya kampaniyi, yemwe anachita mphumi ndikupeza ndalama zochuluka kuposa apa ndi mkulu wina wa ku Ghana, yemwe anapeza ndalama zokwana K843 million.

Related posts

Osewera wakale wa Silver Strikers wamwalira

Romeo Umali

Zipani za ndale azipempha kuti ziyanjane pa mwambo oyika maliro

MBC Online

Prezidenti Chakwera ndi wa masomphenya — Mkaka

Mayeso Chikhadzula
error: All Content is protected. Copyright © 2022. Malawi Broadcasting Corporation. All Right Reserved.