Mnyamata wa zaka 20 wa ku Lilongwe, wapeza mphoto ya ndalama zokwana K174.2 million atasewera masewero oulutsa ndege ndi BetPawa.
Akuluakulu a kampaniyi atsimikiza izi ku Blantyre komwe mwambo olengeza za mnyamatayu unachitika.
Mu mbiri ya kampaniyi, yemwe anachita mphumi ndikupeza ndalama zochuluka kuposa apa ndi mkulu wina wa ku Ghana, yemwe anapeza ndalama zokwana K843 million.