Mwana wa Standard 5 wadzipha atamuletsa kuchita zibwenzi
Mtsikana wazaka 15, Eneles Namusanyo, yemwe anali sitandade 5, wadzipha pokwiya chifukwa chodzudzulidwa khalidwe la zibwenzi. Ofalitsankhani zapolisi ku Mulanje, Innocent Moses, wati mtsikanayo anali

