Tisagulise chimanga chathu chidakali kumunda —Makwangwala
Mfumu yayikulu Makwangwala ya m’boma la Ntcheu yapempha anthu kuti asagulitse mbewu zawo, kuphatikizapo chimanga, isanakwane nthawi yokolola. Mfumuyi yapempha izi potengera kuti alimi ena

