Dr Chakwera adzudzula mchitidwe wa chidodo pa ntchito
Mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera, walangiza atsogoleri a ntchito zosiyanasiyana kuti adzikhala anthu opilira, owonetsa chitsanzo chabwino nthawi zonse komanso kugwira ntchito mwachangu

