‘Osagwiritsa ntchito imfa ya malemu Dr Chilima pa zifukwa za ndale’
Gulu lomwe likuzitcha ‘Mbadwa Zokhudzidwa’ lapempha anthu a ndale kuti asiye kugwiritsantchito imfa ya Dr Saulos Chilima pofuna kumema anthu kuti adziwakonda. M’busa Thoko Banda,

