Olandira mtukula pakhomo agwiritse bwino ntchito ndalama zawo — Boma
Boma lati anthu amene ayamba kulandira ndalama za mtukula pakhomo akhale ndi dongosolo la kagwiritsidwe ntchito ka ndalamazo pofuna kuti miyoyo yawo itukuke ntchitoyi ikamatha.

