Phungu wadera la Mangochi-Makanjira a Benedicto Chambo ati iwo ndi anthu amdera lao lomwe ndi kumpoto kwa boma la Mangochi alipambuyo pa boma la Malawi...
Kukhala nkoke-nkoke pakati pa matimu mu mpikisano wa Champion Kabvina chaka chino pomwe ndalama zomwe matimu amalimbirana zakwera kuchoka pa K13 miliyoni kufika pa K20...
Mtsogoleri wa dziko lino, Dr. Lazarus Chakwera, wati chipata cha Mwanza ndi chofunika kuti kuzikhala malonda zomwe zingathe kubweretsa chitukuko m’Bomali. Chipata-chi ndi chatsopano ndipo...
Gulu la achinyamata a chipani cha Malawi Congress lotchedwa MCP Youth League lapereka katundu osiyana siyana kwa odwala mu chipinda chochilira amai pachipatala chaching’ono cha...
Boma lathetsa mulandu wa anthu atatu omwe anawamanga chifukwa chosokoneza mdipiti wa mtsogoleri wa dziko lino pa HHI mu mzinda wa Blantyre. Mkulu oimira boma...
Adindo a malo ochitira kafukufuku a Chitedze Research Station ku Lilongwe adandaula ndi mchitidwe wodula mitengo omwe akuti ukusokoneza ntchito zina za kafukufuku pa malopa....
Bungwe la Mulakho wa a Lhomwe lati ndi lodabwa ndi mafumu ena omwe sakumvetsa zakusankha kwa mfumu yatsopano ya a Lhomwe Paramount Chief Kaduya. Wapampando...
Bungwe la Malawi Gaming and Lotteries Authority ( MAGLA), lachenjeza kuti lamulo ligwira ntchito kwa makolo omwe amalimbikitsa ana awo kuchita juga. Mkulu wa bungwe...