Africa Local News Nkhani Politics“MALONDA AFUNIKA PA CHIPATA CHA MWANZA” – CHAKWERARomeo UmaliJanuary 27, 2024January 28, 2024 by Romeo UmaliJanuary 27, 2024January 28, 202401556 Mtsogoleri wa dziko lino, Dr. Lazarus Chakwera, wati chipata cha Mwanza ndi chofunika kuti kuzikhala malonda zomwe zingathe kubweretsa chitukuko m’Bomali. Chipata-chi ndi chatsopano ndipo...