Alimi m’boma la Neno ati ali ndi chikhulupiliro kuti ayamba kukolora zochuluka kutsatira upangiri wamakono omwe apeza kudzera mmaphunziro awulimi. Unduna wa za ulimi, kudzera...
President wa dziko lino yemwenso ayimire chipani cha Malawi Congress, Dr Lazarus Chakwera, watsimikizira anthu m’boma la Ntcheu kuti boma limaliza kupaka phula msewu wa...
Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera wati pa sitolo zapa Lizulu pakufunika town yabwino, chipatala chachikulu komanso ofesi yayikulu ya apolisi pofuna kulimbikitsa chitetezo....
Nduna ya za malonda a Vitumbiko Mumba yachenjeza kuti boma sililekelera kuti aMalawi avutike ndi kukwera kwa mitengo ya zinthu kaamba ka anthu ena adyera....
Kampani ya Electricity Supply Corporation of Malawi (ESCOM) yati $21 million yomwe mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chalwera anakatenga ku msonkhano wa COP27 ithandizira...
President Dr Lazarus Chakwera has pledged to continue promoting trade in Nkhata Bay District. He said this during an address at Nkhata Bay boma where...
Ofesi yoyang’anira za chisamaliro cha anthu m’boma la Likoma yati kusowa kwa chidwi cha makolo pa ana awo ndi chimodzi mwa zifukwa zomwe zikukolezera kuti...
Chipani cha National Youth Alliance (NYA) chati mtsogoleri wa chipani cha Malawi Congress (MCP) yemwenso ndi mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazaurus Chakwera ndi yekhayo...
Ntchito yodzipezera malo mu ndime yadziko lonse mumpikisano wa 1 NICO Netball m’chigawo chapakati tsopano yafika pachimake pamene matimu a CIVO Nets ndi Blue Eagles...