Author : Emmanuel Chikonso
365 Posts -
0 Comments
Malawi ndi mgodi wazambiri — SMASE
Bungwe la Strengthening Science and Mathematics Education in Africa (SMASE) lati dziko la Malawi lili ndi kuthekera kokhala mphika waza ulimi mu Africa pokhapokha patakhala...
NGORA yati K1BN ithandiza mabungwe awo kudzidalira
Mabungwe amene si aboma ayamikira boma poyika thumba lapadera la K1 bilion lothandiza ntchito za mabungwewa. Mkulu wa bungwe la Non-Governmental Organisation Regulatory Authority (NGORA),...
Ku Mingoli Bash ilipo 2026 — Kalukusha
Oyendetsa ndi kukonza Ku Mingoli Bash, a Sound Addicts Live, ati mwambowu udzachitika m’chaka cha 2026 m’malo mwa chaka chino ku Cape Maclear m’boma la...
MACRA ikuchita bwino — Suleman
Bungwe la Malawi Communications Regulatory Authority (MACRA) lamema anthu kuti aphunzire kuyamikira bungweli chifukwa likuyesetsa kutukula njira zamakono zofalitsira uthenga komanso kuteteza aMalawi ku uthenga...
Pulezidenti wakale wa FAMA wafunira zabwino Mayi Kingston
Mtsogoleri wakale wa bungwe la Film Association of Malawi (FAMA), a Gift Sukali, wafunira zabwino atsogoleri atsopano amene bungweli lawasankha kumene. A Sukali ati ndi...
‘Pakufunika maphunziro ama award’
Oyendetsa mwambo opereka mphotho wa Maso Awards, a Augastine Mukisi, wati pakufunika aluso alandire maphunziro apadera okhudza miyambo yamtunduwu (awards) kuti athe kumvetsetsa momwe zimayendera....
Premier Bet donates to Police in Lilongwe
Premier Bet Malawi has donated over 150 reflector jackets and a K1 million cheque to Area 3 Police Station to help combat crime during the...