Anthu aku Nsalu ku Lilongwe awalangiza kuti akavotere Dr Lazarus Chakwera pa chisankho cha chaka chino kuti zitukuko zipitilire.
Mlembi wamkulu wa chipani cha Malawi Congress (MCP), yemwenso ndi nduna ya maboma ang’ono, umodzi ndi chikhalidwe, a Richard Chimwendo Banda, ndiye wanena izi ndikulimbikitsa...

