Malawi Broadcasting Corporation
Local Nkhani

Kawale akuyendela ntchito ya Shire Valley Transformation

Nduna ya zaulimi a Sam Kawale lero ikuyendela ntchito yomanaga ngalande yodutsa madzi aulimi wanthilira pansi pa Shire Valley Transformation Program mboma la Chikwawa.

Ndunayi ayifotokozela kusintha komwe kulipo pama plan omanga ngalandeyi kamba ka Namondwe Ana yemwe anakokolola zomangamanga zina za ntchito yi mchaka cha 2022.

Gawo loyamba lomanga ngalandeyi ifika kumapeto mkatikati mwa chaka cha mawa.

 

Olemba Chipiliro Mtumodzi

Related posts

‘AMalawi adzipindula ndi zachikhalidwe’

Romeo Umali

GEFT ichepetsa mavuto obwera ndi kusintha kwa nyengo — Boma, UNDP

Romeo Umali

Committee announces closure Tobacco selling season

Romeo Umali
error: All Content is protected. Copyright © 2022. Malawi Broadcasting Corporation. All Right Reserved.