Oyimba zauzimu tisaike chidwi pa ndalama koma Mulungu – Kamwendo
M’modzi mwa oyimba nyimbo zauzimu m’dziko muno, Ethel Kamwendo, walangiza oyimba nyimbo zauzimu kuti asakomedwe ndi ndalama koma agwiritse maitanidwe awo pomaimba nyimbo zolimbikitsa miyoyo...

