Bus ya timu ya FCB Nyasa Big Bullets yachotsedwa kumalo amene amayisunga, ku bwalo la milandu la Blantyre High Court m’mawa uno.
Bus yi inali kumeneku chifukwa cha ngongole imene timuyi idali nayo ndi mphunzitsi wawo wakale, Franco Ndawa, yomwe ayilipira masiku angapo apitawo.