Malawi Broadcasting Corporation
Local Nkhani

Atsogoleri a zipembedzo alimbikitsa umodzi pa chikumbutso

Atsogoleri azipembedzo zosiyanasiyana alimbikitsa umodzi pakati pa aMalawi, pomwe patha chaka chimodzi dziko lino litakumana ndi namondwe wa Freddy.

Ena mwa alalikiwa ndi Phophet Shepherd Bushiri, M’busa Biswick Nkhoma yemwe ndi Moderator wa  CCAP General Assembly, Sheikh Swalley Chilundu a Muslim Association of Malawi ndi ena.

Iwo athokoza Prezidenti Dr Lazarus Chakwera kamba kopempha thandizo kwa anthu ndi mabungwe kuthandiza dziko lino pa nthawi ya Namondwe.

Iwo apemphanso aMalawi kuti asataye mtima mu nyengo zonse zimene dziko lino lakhala likukumana nazo.

 

Olemba: Blessings Cheleuka

Print Friendly, PDF & Email

Related posts

MCP diaspora wing sees hope in Chakwera’s US visit

MBC Online

Malawi, Uganda and Kenya holding talks on ending child labor

Earlene Chimoyo

Another big winner!

Arthur Chokhotho
error: All Content is protected. Copyright © 2022. Malawi Broadcasting Corporation. All Right Reserved.