Malawi Broadcasting Corporation
Agriculture Business Development Local Local Nkhani

Admarc idzigula chimanga pamtengo okwera

Bungwe la Admarc tsopano lidzigula chimanga pa mtengo wa K700 pa kilogramme (K35,000 pa thumba la 50 kilogrammes), malinga ndi mkulu wa bungweli, a Daniel Makata.

Mtengowu wakwera kuchoka pa K650 pa kilogramme (K32,500 pa thumba lolemera 50 kilogrammes) umene boma linakhazikitsa ngati poyambira.

A Makata ati Admarc yachita izi pofuna kuwonetsetsa kuti alimi akupindula ndi ulimi monga boma likufunira.

 

Print Friendly, PDF & Email

Related posts

Artists still paying Martse homage

MBC Online

ECAM, ILO FOR MORE AWARENESS OF INTERNATIONAL LABOUR STANDARDS

McDonald Chiwayula

Churches promote development — Mwambande

Rudovicko Nyirenda
error: All Content is protected. Copyright © 2022. Malawi Broadcasting Corporation. All Right Reserved.