Mobile Network operator, TNM, has celebrated its strong financial performance and customer growth in 2025 by approving a bonus equivalent to three months salary for...
Bwalo lalikulu lomva milandu yaza chuma ku Blantyre lakana pempho la a Norman Chisale kuti lisinthe mfundo zina pa mlandu umene ukukhudza chuma chimene yemwe...
Prezidenti wa dziko lino, Dr. Lazarus Chakwera ndi Mayi wa dziko lino, Madam Monica Chakwera, ati ndi okhudzika kwambiri ndi imfa ya mtsogoleri wa mpingo...
The Media Council of Malawi (MCM) has urged journalists to prioritise their safety when covering elections. MCM Executive Director Moses Kaufa made the remarks during...
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, Dr Micheal Usi, afika m’dziko muno mawa atakhala nawo pa mwambo olumbilitsa mtsogoleri wa tsopano wa dziko la Mozambique,...
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Dr Michael Usi wati ndi okhumudwa ndi mchitidwe wa anthu ena amene akumaba thandizo la chimanga lomwe Boma likupereka...
Minister of Information and Digitalisation, Moses Kunkuyu, has urged the Anti Corruption Bureau (ACB) to handle corruption cases quickly to instil confidence in Malawians in...
Government says the new national social protection policy will help foster the inclusiveness of persons with disabilities. Ben M’bwana, Director of Administration in the Ministry...
Bungwe lotolera misonkho la Malawi Revenue Authority MRA lati likukumana ndi mavuto pa ntchito yotolera misonkho, maka pa galimoto zimene zimalowa m’dziko muno mozemba. Mkulu...
Bungwe la ESCOM lati makina ake a magetsi anadzithimitsa lero nthawi itatsala mphindi 18 kuti ikwane 12 koloko masana. Malinga ndi chikalata chomwe a ESCOM...