Chepetsani chinyengo poweruza milandu — Mzikamanda
Mkulu wa mabwalo a milandu m’dziko muno, Justice Rizine Mzikamanda, walangiza oweruza milandu mumabwalo osiyanasiyana kuti adzilemekeza malumbiro awo pogwira ntchito yawo mwachilungamo. A Mzikamanda

