Amumanga atanamiza anthu kuti amachulukitsa ndalama m’matsenga
Apolisi ku Limbe munzinda wa Blantyre amanga Rodrick Kaliwo wazaka 28 pomuganizira kuti wakhala akubera anthu powanamiza kuti amachulukitsa ndalama m’matsenga. Kaliwo anamangidwaponso pamulandu ngati

