Ntchito yodinda ma pasipoti yayambiranso ku Mzuzu
Nthambi yoona zolowa ndi kutukuka mdziko muno ya Immigration yalengeza zakuyambanso kwa ntchito yodinda ndikupereka ziphaso zoyendera mchigawo chakumpoto. Malinga ndi chikalata chomwe wasayinira ndi

