Communities in Nsanje have applauded the Climate Smart Enhanced Public Works Program (CSEPWP) for its role in reducing deforestation in the district. Marita William, from
Akuluakulu a ofesi ya zaumoyo ku khonsolo ya boma la Balaka awayamikira polimbikitsa ntchito yoonetsetsa kuti anthu akulandila thandizo la zachipatala mosavuta. Nduna ya za
Mafumu a m’maboma a Mzimba ndi Kasungu asayinira mgwirizano ndi akuluakulu a kampani ya Globe Metals and Mining womwe uthandize kuti anthu a mmadera ozungulira
Akuluakulu a malo ogona alendo a Mount Soche munzinda wa Blantyre ati akwanitsa kuzimitsa moto umene unabuka pamalowo. Malinga ndi mmodzi mwa akuluakuluwo, motowo unabuka
Alimi a ng’ombe za mkaka m’chigawo cha ku m’mwera apempha madalaivala agalimoto zikuluzikulu kuti asiye kunyanyala ntchito chifukwa akutaya mkaka wambiri. Dzulo lokha, alimiwa ati
In a bid to combat maternal mortality, Nation Publication Limited (NPL) is gearing up for its Mother’s Fun Run project, an initiative aimed at ensuring
Nduna yowona za chisamaliro cha anthu a Jean Sendeza yalangiza ogwira ntchito zolemba mayina anthu opindula ndi ndalama za Mtukula Pakhomo mdziko muno kuti aganizire
Brazio Chinthenga has been elected as the new chairperson for Zomba District Council, replacing Baster Chirwa. The council has also elected Everlister Kalimbuka as the
Government has confirmed that 105 community day secondary schools (CDSSs) have been constructed so far across the country under the Secondary Education Expansion for Project