Boma lakhazikitsa gawo lachiwiri la ntchito yolimbikitsa bata ndi mtendere
Boma lakhazikitsa gawo lachiwiri la ntchito yolimbikitsa mtendere komanso kumverana pa mwambo umene unachitikira m’mudzi mwa mfumu yayikulu Mphonde m’boma la Nkhotakota. Komishoni ya Malawi

