Akuluakulu a unduna owona za ngozi zogwa mwadzidzidzi m’dziko la Russia ati ndege ya mtundu wa MI-8T inasowa itangonyamuka kumene pa bwalo la ndege la Vachkazlets ndipo inaynamula anthu okwana 22.
Unduna owona za ngozi zogwa mwadzidzidziwu wati chifunga ndi chomwe chikuchitisa kuti ntchito yosaka ndegeyi ikhale yovuta
By Alufisha Fischer