Wachiwiri kwa mtsogoleri wadziko lino, Dr Micheal Usi, alonjeza kuti apitiriza masomphenya achitukuko a malemu Dr Saulosi Chilima.
Iwo ati agwirizana kale ndi Prezidenti Dr Lazarus Chakwera kuti masomphenya achitukuko a malemu Chilima asafe.
Iwo amayankhula izi kwa khamu limene lawayimitsa pa Kameza ku Blantyre kuti awayankhule.
Olemba: Blessings Cheleuka