Malawi Broadcasting Corporation
Nkhani

Chakwera Wathokoza Livingstonia Synod

President Dr Lazarus Chakwera wathokoza Sinodi ya Livingstonia ya mpingo wa CCAP chifukwa chothandiza boma pa ntchito zosiyanasiyana za chitukuko.

Poyankhula pa mwambo wa mapemphero womwe ukuchitika pa mpingo wa Mchengautuba ku Mzuzu, a Chakwera ayamikira kuti sinodi ikuthandiza mu nthambi za maphunziro, ukhondo komanso kuthetsa njala m’dziko muno.

Iye wati ichi ndi chizindikiro chakuti mpingowu ndi wodzipereka pofuna kuonetsetsa kuti masomphenya a dziko lino a mlozo wa 2063 akwanilitsidwa.

Related posts

Khamu lakonzeka kumva mfundo za chitukuko ku Lilongwe

Romeo Umali

UNICEF ipitiliza kuthandiza Mtukula Pakhomo

Alinafe Mlamba

Giboh Pearson wapulumuka ku ngozi

Romeo Umali
error: All Content is protected. Copyright © 2022. Malawi Broadcasting Corporation. All Right Reserved.